1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 68:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.] 1 Petulo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]
5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+