Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+Amene amakuyang’anira sangawodzere.+ Miyambo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+ Luka 1:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”
10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+
79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”