Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Patukani pa zinthu zoipa ndipo chitani zabwino.+

      Funafunani mtendere ndi kuusunga.+

  • Salimo 37:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Patuka pa choipa ndipo uchite chabwino,+

      Ukatero udzakhala padziko lapansi mpaka kalekale.+

  • Salimo 101:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Sindidzaika maso anga pa chinthu chilichonse chopanda pake.+

      Ndimadana ndi zochita za opatuka pa choonadi.+

      Sindilola kuti zochita zawozo zindikhudze.+

  • Salimo 119:104
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 104 Chifukwa cha malamulo anu ndimachita zinthu mozindikira.+

      N’chifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+

  • Amosi 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+

  • Aroma 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Sindimvetsetsa kuti n’chifukwa chiyani ndimachita zinthu motere. Chifukwa zimene ndimafuna kuchita, sindizichita. Koma zimene ndimadana nazo ndi zimene ndimachita.

  • Aroma 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chikondi+ chanu chisakhale cha chiphamaso.+ Nyansidwani ndi choipa,+ gwiritsitsani chabwino.+

  • Aheberi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Unakonda chilungamo ndipo unadana ndi kusamvera malamulo. N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako, anakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu kuposa cha mafumu ena.”+

  • Yuda 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Apulumutseni+ mwa kuwakwatula pamoto.+ Pitirizaninso kuchitira chifundo ena onse, koma ndi mantha. Iwo aipitsa zovala zawo zamkati ndi ntchito za thupi. Choncho pamene mukuwachitira chifundo, mutalikirane kwambiri ndi zovala zawo zoipitsidwazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena