Salimo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patukani pa zinthu zoipa ndipo chitani zabwino.+Funafunani mtendere ndi kuusunga.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 koma aleke zoipa+ ndipo achite zabwino. Ayesetse kupeza mtendere ndi kuusunga.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+