Salimo 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Patuka pa choipa ndipo uchite chabwino,+Ukatero udzakhala padziko lapansi mpaka kalekale.+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+ Miyambo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usamadzione kuti ndiwe wanzeru.+ Uziopa Yehova ndi kupatuka pa choipa.+ Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+ Amosi 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+ Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi+ chanu chisakhale cha chiphamaso.+ Nyansidwani ndi choipa,+ gwiritsitsani chabwino.+
10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+
15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+