Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+

      Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+

  • Salimo 125:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndodo yachifumu ya oipa sidzapitiriza kukhala+ padziko limene olungama analandira monga cholowa chawo,

      Kuti olungamawo asatambasule dzanja lawo ndi kuchita choipa.+

  • Yeremiya 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Ndidzakulanditsa m’manja mwa anthu oipa+ ndipo ndidzakuwombola m’manja mwa anthu ankhanza.”

  • Danieli 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pamenepo Nebukadinezara anati: “Atamandike Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ amene anatumiza mngelo wake+ ndi kupulumutsa atumiki ake amene anamudalira+ ndiponso amene sanamvere mawu a mfumu, koma anali okonzeka kufa chifukwa sanafune kutumikira+ ndi kulambira+ mulungu wina aliyense kupatulapo Mulungu wawo.+

  • Mateyu 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena