Miyambo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofesa zosalungama adzakolola zopweteka,+ ndipo ndodo ya ukali wake idzatha.+ Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake. Yesaya 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wathyola ndodo ya anthu oipa, ndodo ya anthu olamulira,+
5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake.