Salimo 125:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndodo yachifumu ya oipa sidzapitiriza kukhala+ padziko limene olungama analandira monga cholowa chawo,Kuti olungamawo asatambasule dzanja lawo ndi kuchita choipa.+
3 Ndodo yachifumu ya oipa sidzapitiriza kukhala+ padziko limene olungama analandira monga cholowa chawo,Kuti olungamawo asatambasule dzanja lawo ndi kuchita choipa.+