Mateyu 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ 1 Akorinto 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira. Chivumbulutso 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+
41 Khalani maso+ ndipo pempherani+ kosalekeza kuti musalowe m’mayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira.
10 Popeza unasunga mawu onena za kupirira kwanga,+ inenso ndidzakusunga+ pa ola la kuyesedwa, limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakusunga pa ola limene likubwera kudzayesa okhala padziko lapansi.+