Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ pakuti simukudziwa pamene nthawi yoikidwiratu idzafika.+ 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+ Chivumbulutso 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani maso.+ Mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda uku ndi uku ngati mkango wobangula, wofunitsitsa kuti umeze winawake.+
15 “Taona! Ndikubwera ngati mbala.+ Wodala ndi amene akhalabe maso+ ndi kukhalabe chivalire malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu n’kuona maliseche ake.”+