Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+ Luka 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iye anawauza kuti: “Mukugona chifukwa chiyani? Dzukani, pitirizani kupemphera kuti musalowe m’mayesero.”+
46 Iye anawauza kuti: “Mukugona chifukwa chiyani? Dzukani, pitirizani kupemphera kuti musalowe m’mayesero.”+