Maliko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Amuna inu, khalani maso ndipo muzipemphera,+ kuti musalowe m’mayesero. Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Aroma 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ndimaona chilamulo china m’ziwalo zanga+ chikumenyana+ ndi chilamulo cha m’maganizo mwanga+ n’kundipanga kukhala kapolo wa chilamulo cha uchimo+ chimene chili m’ziwalo zanga. Agalatiya 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti zilakolako za thupi zimalimbana ndi mzimu,+ mzimunso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana, choncho zinthu zimene mumafuna kuchita simuzichita.+
38 Amuna inu, khalani maso ndipo muzipemphera,+ kuti musalowe m’mayesero. Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
23 koma ndimaona chilamulo china m’ziwalo zanga+ chikumenyana+ ndi chilamulo cha m’maganizo mwanga+ n’kundipanga kukhala kapolo wa chilamulo cha uchimo+ chimene chili m’ziwalo zanga.
17 Pakuti zilakolako za thupi zimalimbana ndi mzimu,+ mzimunso umalimbana ndi thupi. Zinthu ziwiri zimenezi zimatsutsana, choncho zinthu zimene mumafuna kuchita simuzichita.+