Maliko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+