Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa,*+ koma mutiteteze kwa woipayo.’+ Luka 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo mutikhululukire machimo athu,+ chifukwa nafenso timakhululukira aliyense amene amatilakwira.*+ Komanso tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa.’”*+ Luka 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iye anawauza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona? Dzukani ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+
4 Ndipo mutikhululukire machimo athu,+ chifukwa nafenso timakhululukira aliyense amene amatilakwira.*+ Komanso tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa.’”*+
46 Iye anawauza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona? Dzukani ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+