Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+ Luka 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo mutikhululukire machimo athu,+ pakuti nafenso timakhululukira aliyense amene amatilakwira.*+ Komanso musatilowetse m’mayesero.’”+
4 Ndipo mutikhululukire machimo athu,+ pakuti nafenso timakhululukira aliyense amene amatilakwira.*+ Komanso musatilowetse m’mayesero.’”+