Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Maliko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+ Akolose 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngati wina ali ndi chifukwa chodandaulira+ za mnzake. Monga Yehova* anakukhululukirani+ ndi mtima wonse, inunso teroni.
25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+
32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+
13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngati wina ali ndi chifukwa chodandaulira+ za mnzake. Monga Yehova* anakukhululukirani+ ndi mtima wonse, inunso teroni.