Mateyu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mukamakhululukira anthu machimo awo, inunso Atate wanu wakumwamba adzakukhululukirani.+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+ Akolose 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngati wina ali ndi chifukwa chodandaulira+ za mnzake. Monga Yehova* anakukhululukirani+ ndi mtima wonse, inunso teroni.
32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+
13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngati wina ali ndi chifukwa chodandaulira+ za mnzake. Monga Yehova* anakukhululukirani+ ndi mtima wonse, inunso teroni.