Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+ Danieli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imvani, inu Yehova.+ Tikhululukireni, inu Yehova.+ Timvereni ndipo muchitepo kanthu,+ inu Yehova. Inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu musazengereze,+ pakuti mzinda wanu ndi anthu anu amatchedwa ndi dzina lanu.”+ Mateyu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+
9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
19 Imvani, inu Yehova.+ Tikhululukireni, inu Yehova.+ Timvereni ndipo muchitepo kanthu,+ inu Yehova. Inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu musazengereze,+ pakuti mzinda wanu ndi anthu anu amatchedwa ndi dzina lanu.”+
6 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo+ . . .” pamenepo anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+