Maliko 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma kuti anthu inu mudziwe kuti Mwana wa munthu+ ali ndi mphamvu zokhululukira machimo padziko lapansi,”+ . . . anauza wakufa ziwalo uja kuti: Luka 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo . . .” anauza munthu wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+
10 Koma kuti anthu inu mudziwe kuti Mwana wa munthu+ ali ndi mphamvu zokhululukira machimo padziko lapansi,”+ . . . anauza wakufa ziwalo uja kuti:
24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo . . .” anauza munthu wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga kabedi kakoka uzipita kwanu.”+