2 Mbiri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+ Amosi 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chilungamo chiyende ngati madzi+ ndiponso ngati mtsinje wosaphwa nthawi zonse.+
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Samalani zochita zanu+ chifukwa simukuweruzira munthu koma mukuweruzira Yehova,+ ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+