Deuteronomo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamakondere poweruza.+ Munthu wamba ndi munthu wolemekezeka onse muziwamvetsera chimodzimodzi.+ Musamaope munthu+ chifukwa mukuweruzira Mulungu.+ Mlandu umene wakuvutani muziubweretsa kwa ine kuti ndiumve.’+ Salimo 82:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Mulungu waima pakati pa msonkhano wake,+Ndipo akuweruza pakati pa milungu kuti:+
17 Musamakondere poweruza.+ Munthu wamba ndi munthu wolemekezeka onse muziwamvetsera chimodzimodzi.+ Musamaope munthu+ chifukwa mukuweruzira Mulungu.+ Mlandu umene wakuvutani muziubweretsa kwa ine kuti ndiumve.’+