Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Amenewa ndiwo aziweruza anthu pa nkhani iliyonse yoyenera. Ndiyeno pakakhala nkhani iliyonse yaikulu azibwera nayo kwa iwe,+ koma nkhani iliyonse yaing’ono, iwo monga oweruza aziisamalira. Choncho amunawo athandizane nawe kunyamula mtolowu, kuti udzipeputsire ntchito.+

  • Salimo 82:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 “Ine ndanena kuti, ‘Inu ndinu milungu,+

      Ndipo nonsenu ndinu ana a Wam’mwambamwamba.+

  • Yohane 10:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ngati anthu amene anatsutsidwa ndi mawu a Mulungu anawatcha ‘milungu,’+ ndipo Malemba satha mphamvu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena