Yohane 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo chanu sanalembemo+ kuti, ‘Ine ndinati: “Inu ndinu milungu”’?+ 1 Akorinto 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+
34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo chanu sanalembemo+ kuti, ‘Ine ndinati: “Inu ndinu milungu”’?+
5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+