Ekisodo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakondere munthu wosauka pa mlandu wake.+ Yakobo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mumasankhana pakati panu+ ndipo mwakhala oweruza+ opereka zigamulo zoipa,+ si choncho kodi?