Deuteronomo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+ Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma. Yohane 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndikati ndiweruze, chiweruzo changa chimakhala cholungama, chifukwa sindiweruza ndekha, pakuti Atate amene anandituma ali ndi ine.+
16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+
30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.
16 Koma ndikati ndiweruze, chiweruzo changa chimakhala cholungama, chifukwa sindiweruza ndekha, pakuti Atate amene anandituma ali ndi ine.+