Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+ Yohane 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+
10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+
32 Taonani! Nthawi ikubwera, ndipo yafika kale. Mubalalika aliyense kupita kunyumba kwake,+ ndipo mundisiya ndekha. Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+