Yohane 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndithu ndikukuuzani, nthawi ikubwera ndipo yafika kale, pamene nonse mubalalika, aliyense kupita kunyumba kwake ndipo mundisiya ndekha.+ Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+
32 Ndithu ndikukuuzani, nthawi ikubwera ndipo yafika kale, pamene nonse mubalalika, aliyense kupita kunyumba kwake ndipo mundisiya ndekha.+ Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+