Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+
30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+