Salimo 82:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chitirani chilungamo anthu onyozeka ndi ana amasiye.*+Chitirani chilungamo anthu osautsika ndi osauka.+ Salimo 112:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wachisomo+ komanso wokongoza ena zinthu ndi wabwino.+ י [Yohdh]Amachita zinthu mwachilungamo.+
3 Chitirani chilungamo anthu onyozeka ndi ana amasiye.*+Chitirani chilungamo anthu osautsika ndi osauka.+
5 Munthu wachisomo+ komanso wokongoza ena zinthu ndi wabwino.+ י [Yohdh]Amachita zinthu mwachilungamo.+