Deuteronomo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo+ kapena mlandu wa mwana wamasiye,*+ ndipo usalande mkazi wamasiye chovala chake monga chikole.+ Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+
17 “Usapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo+ kapena mlandu wa mwana wamasiye,*+ ndipo usalande mkazi wamasiye chovala chake monga chikole.+
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+