Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Samala kuti usalankhule mawu achabe mumtima mwako+ kuti, ‘Chaka cha 7, chaka choti anthu angongole amasuke chayandikira,’+ kuti usaolowere manja m’bale wako wosaukayo,+ osam’patsa kalikonse. Pamenepo iye adzafuulira Yehova chifukwa cha zimene iweyo wam’chitira+ ndipo udzapezeka kuti wachimwa.+

  • Yoswa 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Tsopano khalani olimba mtima kwambiri,+ kuti musunge ndi kuchita zonse zimene zinalembedwa m’buku+ la chilamulo cha Mose, posapatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere.+

  • Salimo 40:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+

      Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,

      Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena