Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+ Miyambo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usawonjezere kanthu pa mawu ake+ kuti angakudzudzule ndiponso kuti ungakhale wabodza.+
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+