Deuteronomo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo inu Aisiraeli, muzimvetsera ndi kutsatira mfundo ndi malamulo ake mosamala,+ kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ ndi kuti muchuluke kwambiri m’dziko loyenda mkaka ndi uchi, monga mmene Yehova Mulungu wa makolo anu anakulonjezerani.+ Deuteronomo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo tikatsatira malamulo onsewa monga mmene Yehova Mulungu wathu watilamulira,+ ndiye kuti tikuchita chilungamo+ pamaso pake.’ Deuteronomo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndi kuti muchulukanedi, n’kupita kukatenga dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.+
3 Ndipo inu Aisiraeli, muzimvetsera ndi kutsatira mfundo ndi malamulo ake mosamala,+ kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ ndi kuti muchuluke kwambiri m’dziko loyenda mkaka ndi uchi, monga mmene Yehova Mulungu wa makolo anu anakulonjezerani.+
25 Ndipo tikatsatira malamulo onsewa monga mmene Yehova Mulungu wathu watilamulira,+ ndiye kuti tikuchita chilungamo+ pamaso pake.’
8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndi kuti muchulukanedi, n’kupita kukatenga dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.+