Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ 2 Mafumu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindidzachititsanso phazi la Isiraeli kuchoka panthaka imene ndinapatsa makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ ndiponso mogwirizana ndi chilamulo chonse chimene Mose mtumiki wanga anawalamula.”
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
8 Sindidzachititsanso phazi la Isiraeli kuchoka panthaka imene ndinapatsa makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ ndiponso mogwirizana ndi chilamulo chonse chimene Mose mtumiki wanga anawalamula.”