8 Sindidzachotsanso phazi la Isiraeli panthaka imene ndinapatsa+ makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ ndiponso mogwirizana ndi chilamulo+ chonse, malangizo+ onse, ndi zigamulo+ zonse zimene ndinawapatsa kudzera m’manja mwa Mose.”+