Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+ 2 Samueli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo+ ndi kuwakhazika+ pamalowo. Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama sadzawasautsanso ngati mmene anachitira poyamba,+
23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+
10 Ndipo anthu anga Aisiraeli ndidzawasankhira malo+ ndi kuwakhazika+ pamalowo. Iwo adzakhaladi kumeneko ndipo sadzasokonezedwanso. Anthu osalungama sadzawasautsanso ngati mmene anachitira poyamba,+