Ekisodo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yehova anamuuza Mose ali ku Midiyani kuti: “Nyamuka, bwerera ku Iguputo, chifukwa onse amene anali kufuna moyo wako anafa.”+ Ekisodo 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imene analankhula ndi Farao, Mose anali ndi zaka 80 ndipo Aroni anali ndi zaka 83.+ Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
19 Ndiyeno Yehova anamuuza Mose ali ku Midiyani kuti: “Nyamuka, bwerera ku Iguputo, chifukwa onse amene anali kufuna moyo wako anafa.”+
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.