Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ 1 Mafumu 8:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 (popeza iwo ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa ku Iguputo,+ kuwachotsa m’ng’anjo yachitsulo).+ Nehemiya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+ Salimo 107:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+
51 (popeza iwo ndi anthu anu ndi cholowa chanu,+ amene munawatulutsa ku Iguputo,+ kuwachotsa m’ng’anjo yachitsulo).+
9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+
19 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo.+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+