Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+ Nehemiya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ndi atumiki anu+ ndi anthu anu,+ amene munawawombola ndi mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+
10 Iwo ndi atumiki anu+ ndi anthu anu,+ amene munawawombola ndi mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+