Deuteronomo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero. Salimo 106:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+Kuti mphamvu zake zidziwike.+
20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero.