Yoswa 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+ Salimo 143:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+ Ezekieli 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa mitundu ya anthu amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+
9 Akanani ndi anthu onse a m’dziko lino adzamva zimenezi, ndipo adzatizinga ndithu, ndi kufafaniza dzina lathu kulichotsa padziko lapansi.+ Nanga zikatero mudzaliteteza bwanji dzina lanu lalikulu?”+
11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+
14 Koma ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa mitundu ya anthu amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+