Ekisodo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka. Deuteronomo 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+ Salimo 106:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+Kuti mphamvu zake zidziwike.+ Salimo 143:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+ Ezekieli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene iwo anali kukhala pakati pawo,+ pakuti ndinawachititsa kuti andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo powatulutsa m’dziko la Iguputo.+
12 Aiguputo+ anenerenji kuti, ‘Anawatulutsa m’dziko lino kuti akawaphe kumapiri ndi kuwafafaniza padziko lapansi’?+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo,+ ndipo mverani chisoni+ anthu anu kuti musawagwetsere tsoka.
27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+
11 Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo+ chifukwa cha dzina lanu.+Chotsani moyo wanga m’masautso+ monga mwa chilungamo chanu.+
9 Koma ine ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene iwo anali kukhala pakati pawo,+ pakuti ndinawachititsa kuti andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo powatulutsa m’dziko la Iguputo.+