Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+ Salimo 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndathawira kwa inu Yehova.+Musalole kuti ndichite manyazi.+Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+
31 Ndathawira kwa inu Yehova.+Musalole kuti ndichite manyazi.+Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+