Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+

  • Salimo 85:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choonadi chidzaphuka padziko lapansi,+

      Ndipo chilungamo chidzayang’ana pansi kuchokera kumwamba.+

  • Salimo 96:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti iye wabwera.+

      Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+

      Adzaweruza dziko mwachilungamo,+

      Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+

  • Yesaya 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena