Salimo 85:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choonadi chidzaphuka padziko lapansi,+Ndipo chilungamo chidzayang’ana pansi kuchokera kumwamba.+ Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+ Yesaya 61:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+