Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Aroma 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nanga ngati ena sanasonyeze chikhulupiriro,+ kodi chifukwa chakuti alibe chikhulupiriro+ ndiye kuti kukhala wokhulupirika kwa Mulungu n’kopanda pake?+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
3 Nanga ngati ena sanasonyeze chikhulupiriro,+ kodi chifukwa chakuti alibe chikhulupiriro+ ndiye kuti kukhala wokhulupirika kwa Mulungu n’kopanda pake?+