2 Atesalonika 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzitero kutinso tilanditsidwe kwa anthu opweteka anzawo ndi oipa,+ pakuti chikhulupiriro sichikhala ndi anthu onse.+ Aheberi 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ monga mmenenso unalengezedwera kwa makolo athu.+ Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo,+ chifukwa sanakhale ndi chikhulupiriro+ ngati cha amene anamvera mawuwo.+
2 Muzitero kutinso tilanditsidwe kwa anthu opweteka anzawo ndi oipa,+ pakuti chikhulupiriro sichikhala ndi anthu onse.+
2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ monga mmenenso unalengezedwera kwa makolo athu.+ Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo,+ chifukwa sanakhale ndi chikhulupiriro+ ngati cha amene anamvera mawuwo.+