Aheberi 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ ngati mmenenso anaulengezera kwa makolo athu. Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo, chifukwa analibe chikhulupiriro chofanana ndi cha amene anamvera mawuwo.
2 Uthenga wabwino unalengezedwa kwa ife,+ ngati mmenenso anaulengezera kwa makolo athu. Koma mawu amene iwo anamva sanapindule nawo, chifukwa analibe chikhulupiriro chofanana ndi cha amene anamvera mawuwo.