7 Atatsutsana kwambiri za nkhaniyi, Petulo anaimirira nʼkuwauza kuti: “Abale anga, mukudziwa bwino kuti mʼmasiku oyambirira Mulungu anandisankha ine pakati panu, kuti kudzera pakamwa panga, anthu a mitundu ina amve mawu a uthenga wabwino nʼkukhulupirira.+