1 Akorinto 15:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+ Aheberi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa timachita nawo zimene Khristu akuchita, ngati zinthu zimene tinkadalira poyamba tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+
58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+
14 Chifukwa timachita nawo zimene Khristu akuchita, ngati zinthu zimene tinkadalira poyamba tazigwira mwamphamvu mpaka mapeto.+